Silent night in Chichewa

Usikuwo woyerawo
Mwana adamlerayo
Akakhale Mfumuyo
Anabadwa m'kholamo,
Mfumu ya mafumo
Ndi ya anthuwo.

Mwanayo wa Mulunguyo
Andikonda inetu,
Nan'tayira chumacho
Nadzagona m'udzumo.
Ndiyamika Mbuye
Wanga Yesuyo.

Usikuwo woyerawo!
Wadzatu mtenderewo
Ife tonse anthuwo
Atitenga Mlunguyo.
Mlemekeze 'Tate,
Mwana, Mzimunso.

Christmas Yabwino!

(Thanks Soyapi!)

0 Response to Silent night in Chichewa

Post a Comment